Levitiko 17:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wansembeyo awaze mwaziwo pa guwa la nsembe la Yehova, pa khomo la cihema cokomanako, natenthe mafuta akhale pfungo lokoma lokwera kwa Yehova.

Levitiko 17

Levitiko 17:1-11