Levitiko 15:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wakukhayo akalabvulira wina woyera; pamenepo atsuke zobvala zace, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.

Levitiko 15

Levitiko 15:1-16