Levitiko 15:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mose ndi Aroni, nati,

2. Nenani nao ana a Israyeli, nimuti nao, Pamene mwamuna ali yense ali ndi nthenda yakukha m'thupi mwace, akhale wodetsedwa, cifukwaca kukha kwace.

Levitiko 15