Levitiko 13:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Masiku onse nthenda ikali pa iye azikhala wodetsedwa; ali wodetsedwa, agone pa yekha pokhala pace pakhale kunja kwa cigono.

Levitiko 13

Levitiko 13:43-52