Levitiko 10:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo ana a Aroni, Nadabu ndi Abihu anatenga yense mbale yace ya zofukiza, naikamo moto, naikapo cofukiza, nabwera nao pamaso pa Yehova moto wacilendo, umene sanawauza.

2. Ndipo panaturuka moto pamaso pa Yehova, nuwatha, nafa iwo pamaso pa Yehova.

Levitiko 10