Hoseya 5:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Imvani ici, ansembe inu; mverani, inu nyumba ya Israyeli; cherani khutu, inu nyumba ya mfumu; pakuti ciweruzoci cinena inu; pakuti munakhala msampha ku Mizipa, ndi ukonde woyalidwa pa Tabora.

2. Ndipo opandukawo analowadi m'zobvunda; koma Ine ndine wakuwadzudzula onsewo.

Hoseya 5