Hoseya 14:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzakhala kwa Israyeli ngati mame; adzacita maluwa ngati kakombo, ndi kutambalalitsa mizu yace ngati Lebano.

Hoseya 14

Hoseya 14:1-9