Hoseya 12:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi Gileadi ndiye wopanda pace? akhala acabe konse; m'Giligala aphera nsembe yang'ombe; inde maguwa ao a nsembe akunga miulu yamiyala m'micera ya munda.

Hoseya 12

Hoseya 12:10-14