Habakuku 3:18-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Koma ndidzakondwera mwa Yehova,Ndidzasekerera mwa Mulungu wa cipulumutso canga.

19. Yehova, Ambuye, ndiye mphamvuyanga,Asanduliza mapazi anga ngati a mbawala,Nadzandipondetsa pa misanje yanga.

Habakuku 3