Genesis 48:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

mthenga amene anandiombola ine ku zoipa zonse, adalitse anyamatawa; dzina langa lichulidwe pa iwo, ndi dzina la makolo anga Abrahamu ndi Isake; iwo akule, nakhale khamu pakati pa dziko lapansi.

Genesis 48

Genesis 48:6-22