Genesis 44:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nuike cikho canga, cikho casiliva ciija, kukamwa kwa thumba la wamng'ono, pamodzi ndi ndalama za tirigu zace. Ndipo iye anacita monga mau ananena Yosefe.

Genesis 44

Genesis 44:1-4