Genesis 42:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yakobo sanamtuma Benjamini mphwace wa Yosefe, pamodzi ndi abale ace, cifukwa anati, Coipa cingamgwere iye.

Genesis 42

Genesis 42:1-7