Genesis 42:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anati wina ndi mnzace, Tacimwiratu mbale wathu, pamene tinaona kubvutidwa kwa mtima wace, potipembedzera ife, koma ife tinakana kumvera, cifukwa cace kubvutidwa kumene kwatifikira.

Genesis 42

Genesis 42:16-28