Genesis 41:51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anamucha dzina la woyamba Manase, cifukwa anati iye, Mulungu wandiiwalitsa ine zobvuta zanga zonse, ndi nyumba yonse ya atate wanga.

Genesis 41

Genesis 41:45-57