Genesis 41:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Farao anacotsa mphete yosindikizira yace pa dzanja lace, naibveka pa dzanja la Yosefe, nambveka iye ndi zobvalira zabafuta, naika unyolo wagolidi pakhosi pace;

Genesis 41

Genesis 41:39-47