Genesis 41:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ng'ombe zazikazi zisanu ndi ziwiri zabwino ndizo zaka zisanu ndi ziwiri, ndi ngala zisanu ndi ziwiri zabwino ndizo zaka zisanu ndi ziwiri: loto liri limodzi.

Genesis 41

Genesis 41:20-28