Genesis 4:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa iye, Cifukwa cace ali yense amene adzapha Kaini kudzabwezedwa kwa iye kasanu ndi kawiri. Ndipo Yehova anaika icizindikiro pa Kaini, kuti asamuphe ali yense akampeza.

Genesis 4

Genesis 4:6-18