Genesis 38:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali pamene iye ana bweza dzanja lace, kuti, taona, mbale wace anabadwa, ndipo namwino anati, Wadziposolera wekha bwanji? cifukwa cace dzina lace linachedwa Pereze.

Genesis 38

Genesis 38:24-30