Genesis 36:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ana amuna a Oholibama mwana wamkazi wa Ana, mwana wamkazi wa Zibeoni, mkazi wace wa Esau, ndi awa: ndipo iye anambalira Esau Jeusi, ndi Jalamu, ndi Kora.

Genesis 36

Genesis 36:8-22