Genesis 35:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anafa Debora mlezi wa Rebeka, naikidwa kunsi kwa Beteli, pansi pa mtengo wathundu; ndipo anacha dzina lace AlioniBakuti.

Genesis 35

Genesis 35:1-9