Genesis 31:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atate wanu wandinyenga ine, nasinthanitsa malipilo anga kakhumi; koma Mulungu sanamlole iye andicitire ine coipa.

Genesis 31

Genesis 31:1-8