Genesis 29:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anamkonda Rakele, nati, Ndidzakutumikirani inu zaka zisanu ndi ziwiri cifukwa ca Rakele mwana wanu wamkazi wamng'ono.

Genesis 29

Genesis 29:12-19