Genesis 28:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiponso kuti pamene anamdalitsa iye, anamuuza iye kuti, Usatenge mkazi wa ana akazi a Kanani; ndiponso kuti Yakobo anamvera atate wace ndi amace, nanka ku Padanaramu;

Genesis 28

Genesis 28:1-12