Genesis 24:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo iye akati kwa ine, Imwatu iwe, ndiponso ndidzatungira ngamila zako; yemweyo akhale mkazi amene Yehova wamsankhira mwana wa mbuyanga.

Genesis 24

Genesis 24:43-47