Genesis 23:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Zitatha izi Abrahamu anaika Sara mkazi wace m'phanga la munda wa Makipela patsogolo pa Mamre (ndiwo Hebroni), m'dziko la Kanani.

20. Ndipo ana a Heti analimbitsira Abrahamu munda, ndi phanga liri m'menemo, likhale lace lamanda.

Genesis 23