Genesis 22:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abrahamu analawira m'mamawa namanga buru wace, natengako anyamata ace awiri pamodzi naye, ndi Isake mwana wace, nawaza nkhuni za nsembe, nauka, nanka kumalo komwe Mulungu anamuuza iye,

Genesis 22

Genesis 22:2-13