Genesis 21:33-34 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndipo Abrahamu ananka mtengo wabwemba pa Beereseba, naitanira pamenepo dzina la Yehova, Mulungu wa nthawi zonse.