Genesis 2:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo zinatha kupangidwa zakumwamba ndi dziko lapansi, ndi khamu lao lonse.

2. Tsiku lacisanu ndi ciwiri Mulungu anamariza nchito yonse anaipanga; ndipo anapuma tsiku lacisanu ndi ciwiri ku nchito yace yonse.

Genesis 2