Genesis 19:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Loti anabwera kuturuka m'Zoari nakhala m'phiri ndi ana akazi awiri pamodzi naye: cifukwa anaopa kukhala m'Zoari, ndipo anakhata m'phanga, iye ndi ana ace akazi.

Genesis 19

Genesis 19:22-33