Genesis 18:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kapena akaperewera asanu pa olungama makumi asanuwo; kodi mudzaononga mudzi wonse cifukwa ca kuperewera asanu? Ndipo anati, Ndikapeza makumi anai ndi asanu sindidzauononga.

Genesis 18

Genesis 18:19-31