Genesis 16:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye adzakhala munthu wa m'thengo; ndipo dzanja lace lidzakhala lotsutsana ndi anthu onse, ndi manja a anthu onse adzakhala otsutsana naye: ndipo iye adzakhala pamaso pa abale ace onse.

Genesis 16

Genesis 16:2-16