Ezekieli 7:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsopano kwakudzera kutha kwako, ndipo ndidzakutumizira mkwiyo wanga, ndi kukuweruza monga mwa njira zako, ndipo ndidzakubwezera zonyansa zako zanse.

Ezekieli 7

Ezekieli 7:2-4