Ezekieli 48:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ku malire a Gadi, mbali ya kumwela, kuloza kumwela, malire akhale kuyambira ku Tamara kufikira ku madzi a Meribati ndi Kadesi, ku mtsinje wa Aigupto, kufikira ku nyanja yaikuru.

Ezekieli 48

Ezekieli 48:26-35