Ezekieli 48:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kunena za mafuko otsala tsono, kuyambira ku mbali ya kum'mawa kufikita mbali ya kumadzulo, Benjamini akhale nalo gawo limodzi.

Ezekieli 48

Ezekieli 48:22-27