Ezekieli 47:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mbali ya kum'mawa pakati pa Haurani, ndi Damasiko, ndi Gileadi, ndi dziko la Israyeli, ndiwo Yordano; muyese kuyambira malire a kumpoto kufikira nyanja ya kum'mawa. Ndiyo mbali ya kum'mawa.

Ezekieli 47

Ezekieli 47:12-21