Ezekieli 44:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo asayandikire kwa munthu ali yense wakufa, angadzidetse; koma cifukwa ca atate, kapena mai, kapena mwana wamwamuna, kapena mwana wamkazi, kapena mbale, kapena mlongo wopanda mwamuna, nkuloleka kudzidetsa.

Ezekieli 44

Ezekieli 44:23-28