Ezekieli 42:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anaturuka nane kumka ku bwalo la kunja, njira ya kumpoto; nalowa nane ku nyumba yazipinda idali pandunji pa mpatawo, ndi pandunji pa nyumbayo inaloza kumpoto.

Ezekieli 42

Ezekieli 42:1-5