Ezekieli 40:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananditsogolera kumka kumwela, ndipo taonani, panali cipata kumwela, nayesa makhoma a pakati pace, ndi zidundumwa zace, monga mwa miyeso yomweyi.

Ezekieli 40

Ezekieli 40:23-34