Ezekieli 39:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wao, popeza ndinalola atengedwe ndende kumka kwa amitundu, koma ndinawasonkhanitsanso akhale m'dziko lao, osasiyakonso mmodzi yense wa iwowa.

Ezekieli 39

Ezekieli 39:25-29