Ezekieli 36:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati nkhosa za nsembe, ngati nkhosa za ku Yerusalemu pa madyerero ace oikika, momwemo midzi yamabwinja idzadzala nao magulu a anthu; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Ezekieli 36

Ezekieli 36:34-38