Ezekieli 30:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku ilo mithenga idzaturuka pamaso panga m'zombo kuopsa Akusi osalabadira; ndipo kudzakhala kuwawa kwakukuru pakati pao, monga tsiku la Aigupto, pakuti taona, likudza.

Ezekieli 30

Ezekieli 30:5-15