Ezekieli 30:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Anandidzeranso mau a Yehova, akuti,

2. Wobadwa ndi munthu iwe, nenera, uziti, Atero Ambuye Yehova, Liritsani, Ha, tsikulo

3. Pakuti layandikira tsiku, layandikira tsiku la Yehova, tsiku lamitambo, ndiyo nyengo ya amitundu.

Ezekieli 30