Ezekieli 28:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndidzatumiza mliri ndi mwazi ilowe m'makwalala ace, ndi olasidwa adzagwa m'kati mwace ndi lupanga lougwera pozungulira ponse; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Ezekieli 28

Ezekieli 28:18-26