16. cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Taona ndidzatambasulira Afilisti dzanja langa, ndi kulikha. Akereti, ndi kuononga otsalira mphepete mwa nyanja.
17. Ndipo ndidzawabwezera cilango cacikuru, ndi malango ankharwe; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, pakuwabwezera cilango Ine.