Ezekieli 23:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero ndidzakuleketsera coipa cako, ndi cigololo cako cocokera m'dziko la Aigupto; ndipo sudzazikwezeranso maso ako, kapena kukumbukiranso Aigupto,

Ezekieli 23

Ezekieli 23:19-28