Ezekieli 22:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Anandidzeransomau a Yehova, akuti,

2. Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, udzaweruza, udzauweruza mudziwo wa mwazi kodi? uudziwitse tsono zonyansa zace zonse.

3. Nuziti, Atero Ambuye Yehova, Ndiwo mudzi wokhetsa mwazi pakati pace, kuti nthawi yace ifike, nudzipangire mafano kudzidetsa nao.

Ezekieli 22