Ezekieli 21:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'dzanja lace lamanja muli ula wa ku Yerusalemu, kuika zogundira, kutsegula pakamwa pa kupha, kukweza mau ndi kupfuula, kuikira zitseko zogundira, kuundira mtumbira, kumanga malinga.

Ezekieli 21

Ezekieli 21:13-25