Ezekieli 21:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wobadwa ndi munthu iwe, nenera, nuombe manja, lupanga lipitirize katatu, lupanga la wolasidwa ndilo lupanga la wolasidwa wamkuruyo, limene liwazinga.

Ezekieli 21

Ezekieli 21:11-21