Ezekieli 12:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wobadwa ndi munthu iwe, udye mkate wako ndi kunthunthumira, ndi kumwa madzi ako ndi kunjenjemera, ndi kutenga nkhawa;

Ezekieli 12

Ezekieli 12:9-20