Ezekieli 12:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndidzawasiya owerengeka apulumuke lupanga, ndi njala, ndi mliri, kuti afotokoze zonyansa zao kwa amitundu kumene afikako; ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Ezekieli 12

Ezekieli 12:7-25